Jeremiah 48:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“A ku Hesiboni ndi a ku Eleale akulira movutika. Kulira kwao kukumveka mpaka ku Yaza, kuchokera ku Zowari mpaka ku Horonaimu ndi ku Egilati-Selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu aphwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuyambira kufuula kwa Hesiboni mpaka ku Eleyale, mpaka ku Yahazi anakweza mau, kuyambira pa Zowari mpaka ku Horonaimu, ku Egilati-Selisiya; pakuti pa madzi a ku Nimurimu komwe padzakhala mabwinja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“A ku Hesiboni ndi Eleali akulira ndipo mfuwu wawo ukumveka mpaka ku Yahazi, kuchokera ku Zowari mpaka ku Horonaimu ndi ku Egilati Selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu aphwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuyambira kupfuula kwa Hesiboni mpaka ku Eleale, mpaka ku Yahazi anakweza mau, kuyambira pa Zoari mpaka ku Horonaimu, ku Egilati-Selisiya; pakuti pa madzi a ku Nimurimu komwe padzakhala mabwinja.