Jeremiah 48:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Mtundu wina udzachita kuuluka nkudzagwera Mowabu ngati nkhwazi ya mapiko otambalitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova atero: Taonani, adzauluka ngati chiombankhanga, adzamtambasulira Mowabu mapiko ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Mtundu wina udzachita kuwuluka nʼkugwera pa Mowabu ngati chiwombankhanga chimene chatambalitsa mapiko ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova atero: Taonani, adzauluka ngati ciombankhanga, adzamtambasulira Moabu mapiko ace.