Jeremiah 48:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe masiku akutsogolo ndidzambwezeranso ufulu Mowabu,” akutero Chauta. Chiweruzo cha Mowabu chathera pamenepa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndidzabwezanso undende wa Mowabu masiku akumaliza, ati Yehova. Ziweruzo za Mowabu ndi zomwezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Komabe masiku akutsogolo ndidzabwezeranso Mowabu chuma chake,” akutero Yehova. Chiweruzo cha Mowabu chathera pamenepa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndidzabwezanso undende wa Moabu masiku akumariza, ati Yehova. Ziweruzo za Moabu ndi zomwezi.