Jeremiah 48:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inunso mudzagwidwa chifukwa choti munkadalira ntchito zanu ndi chuma chanu. Kemosi, mulungu wanu, adzatengedwa ukapolo, pamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, chifukwa wakhulupirira ntchito zanu ndi chuma chanu, iwenso udzagwidwa; ndipo Kemosi adza kundende, ansembe ake ndi akulu ake pamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza inu munkadalira ntchito zanu ndi chuma chanu, nanunso mudzatengedwa ukapolo, ndipo Kemosi adzapita ku ukapolo, pamodzi ndi ansembe ake ndi akuluakulu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, cifukwa wakhulupirira nchito zanu ndi cuma canu, iwenso udzagwidwa; ndipo Kemosi adza kundende, ansembe ace ndi akuru ace pamodzi.