Jeremiah 48:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mowabu mchenjezeni, chifukwa posachedwa asakazika. Mizinda yake isanduka mabwinja, ikhala yopanda anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Patsani Mowabu mapiko, kuti athawe apulumuke; midzi yake ikhale bwinja, lopanda wokhalamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsineni khutu Mowabu chifukwa adzasakazika; mizinda yake idzasanduka mabwinja, wopanda munthu wokhalamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Patsani Moabu mapiko, kuti athawe apulumuke; midzi yace ikhale bwinja, lopanda wokhalamo.