Jeremiah 49:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuchepetsa pakati pa mitundu yonse, anthu onse adzakunyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, taona, ndakuyesa iwe wamng'ono mwa amitundu, ndi wonyozedwa mwa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndidzakuchepetsani pakati pa anthu a mitundu ina. Mudzakhala anthu onyozeka pakati pa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, caona, ndakuyesa iwe wamng'ono mwa amitundu, ndi wonyozedwa mwa anthu.