Jeremiah 49:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Dziko la Edomu lidzasanduka lochititsa nyansi. Onse odutsamo azidzachita nyansi, nkumatsonya chifukwa cha kuwonongeka kwake koopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Edomu adzakhala chizizwitso; ndipo yense wakupitapo adzazizwa, ndipo adzatsonyera zovuta zake zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Dziko la Edomu lidzasanduka chinthu chochititsa mantha. Onse odutsamo adzadabwa ndi kupukusa mitu yawo chifukwa cha kuwonongeka kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Edomu adzakhala cizizwitso; ndipo yense wakupitapo adzazizwa, ndipo adzatsonyera zobvuta zace zonse.