Jeremiah 49:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe udaonongekera mzinda wa Sodomu ndi wa Gomora pamodzi ndi midzi yake yozungulira, momwemonso sikudzakhalako munthu ndi mmodzi yemwe kumeneko. Palibe ndi mmodzi yemwe wodzayendako kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga m'kupasuka kwa Sodomu ndi Gomora ndi midzi inzake, ati Yehova, munthu aliyense sadzakhala m'menemo, mwana wa munthu aliyense sadzagona m'menemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe anawonongekera Sodomu ndi Gomora, pamodzi ndi mizinda yake yozungulira,” akutero Yehova, “motero palibe munthu amene adzakhala mu Edomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga m'kupasuka kwa Sodomu ndi Gomora ndi midzi inzace, ati Yehova, munthu ali yense sadzakhala m'menemo, mwana wa munthu ali yense sadzagona m'menemo.