Jeremiah 49:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lapansi lidzanjenjemera chifukwa cha kugwa kwao. Kulira kwao kudzamveka mpaka ku Nyanja Yofiira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko lapansi linthunthumira ndi phokoso la kugwa kwao; pali mfuu, phokoso lake limveka pa Nyanja Yofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akadzagwa Edomu padzakhala mfuwu waukulu ndipo dziko lapansi lidzanjenjemera; kulira kwawo kudzamveka mpaka ku Nyanja Yofiira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lapansi linthunthumira ndi phokoso Ija kugwa kwao; pali mpfuu, phokoso lace limveka pa Nyanja Yofiira.