Jeremiah 49:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzinda wotchuka uja wasiyidwa, mzinda wachikondwerero uja!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alekeranji kusiya mudzi wa chilemekezo, mudzi wa chikondwero changa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mzinda wotchuka ndi wachikondwerero uja wasiyidwa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alekeranji kusiya mudzi wa cilemekezo, mudzi wa cikondwero canga?