Jeremiah 49:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zedekiya, mfumu ya ku Yuda, atangoyamba kumene kulamulira, Chauta adalankhula ndi mneneri Yeremiya za Elamu. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a Yehova amene anafika kwa Yeremiya mneneri, onena za Elamu poyamba kulamulira Zedekiya mfumu ya Yuda, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga umene Yehova anapatsa mneneri Yeremiya wonena za Elamu, Zedekiya mfumu ya Yuda atangoyamba kulamulira ndi uwu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a Yehova amene anafika kwa Yeremiya mneneri, onena za Elamu poyamba kulamulira Zedekiya mfumu ya Yuda, kuti,