Jeremiah 49:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe, patsogolo pake ndidzaŵabwezera ufulu anthu a ku Elamu,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma padzaoneka masiku akutsiriza, kuti ndidzabwezanso undende wa Elamu, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Komabe mʼtsogolomo ndidzabwezera anthu a ku Elamu dziko lawo,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma padzaoneka masiku akutsiriza, kuti ndidzabwezanso undende wa Elamu, ati Yehova.