Jeremiah 49:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Dedani bwererani, thaŵani mukakhale ku makwaŵa. Ndithudi ndidzalanga zidzukulu za Esau pa tsiku lake la chiweruzo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thawani inu, bwerani, khalani mwakuya, inu okhala m'Dedani; pakuti ndidzatengera pa iye tsoka la Esau, nthawi yoti ndidzamlanga iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu anthu a ku Dedani, thawani, bwererani ndi kukabisala ku makwalala chifukwa ndidzagwetsa mavuto pa zidzukulu za Esau popeza nthawi yawo ya chiweruzo yafika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thawani inu, bwerani, khalani mwakuya, inu okhala m'Dedani; pakuti ndidzatengera pa iye tsoka la Esau, nthawi yoti ndidzamlanga iye.