Jeremiah 49:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Othyola mphesa akadakwera kwa inu, akadakusiyiraniko mphesa pa nthambi. Mbala zikadafika usiku, bwenzi zitangotengako zofunikira zokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akafika kwa inu akutchera mphesa, sadzasiya mphesa zokunkha? Akafika usiku akuba, adzaononga mpaka kutha?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi anthu othyola mphesa akanafika kwa inu akanakusiyiraniko mphesa pangʼono pokha? Anthu akuba akanafika usiku akanangotengako zimene akuzifuna zokha?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akafika kwa inu akuchera mphesa, sadzasiya mphesa zokunkha? akafika usiku akuba, adzaononga mpaka kutha?