Jeremiah 5:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Israele ndi a ku Yuda onse akhala osakhulupirika kwa Ine,” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti nyumba ya Israele ndi nyumba ya Yuda zinandichitira monyenga kwambiri, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyumba ya Israeli ndi nyumba ya Yuda onse akhala osakhulupirika kotheratu kwa Ine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti nyumba ya Israyeli ndi nyumba ya Yuda zinandicitira monyenga kwambiri, ati Yehova.