Jeremiah 5:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo ankanama ponena za Chauta, ankati, “Mulungu sangatichite kanthu. Choipa sichidzatigwera, sitidzaona nkhondo kapena njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akana Yehova, ndi kuti, Si ndiye; choipa sichidzatifika ife; sitidzaona kapena lupanga kapena njala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwowa ankanama ponena za Yehova kuti, “Yehova sangachite zimenezi! Choyipa sichidzatigwera; sitidzaona nkhondo kapena njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akana Yehova, ndi kuti, Si ndiye; coipa sicidzatifika ife; sitidzaona kapena lupanga kapena njala;