Jeremiah 5:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankhondowo mipaliro yao imapha anthu ambirimbiri, onsewo ndi ngwazi zokhazokha pa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Phodo lao lili ngati manda apululu, onsewo ndiwo olimba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zida zawo za nkhondo zapha anthu ambirimbiri; onsewo ndi ankhondo amphamvu okhaokha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Phodo lao liri ngati manda apululu, onsewo ndiwo olimba.