Jeremiah 5:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulalike kwa ana a Yakobe, mulengeze kwa anthu a ku Yuda kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nenani ichi m'nyumba ya Yakobo, lalikirani m'Yuda, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Lengeza izi kwa ana a Yakobo ndipo mulalikire kwa anthu a ku Yuda kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenani ici m'nyumba ya Yakobo, lalikirani m'Yuda, kuti,