Jeremiah 5:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu ameneŵa ndi okanika ndiponso a mtima waupandu. Adapatuka ndipo adapitiratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthu awa ali ndi mtima woukirana ndi wopikisana; anapanduka nachoka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu awa ndi nkhutukumve ndiponso a mitima yowukira; andifulatira ndipo andisiyiratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anthu awa ali ndi mtima woukirana ndi wopikisana; anapanduka nacoka.