Jeremiah 5:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma zolakwa zanu zaletsetsa zonsezi, ndipo machimo anu akumanitsani zokoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mphulupulu zanu zachotsa zimenezi, ndi zochimwa zanu zakukanitsani inu zinthu zabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma zolakwa zanu zalepheretsa zonsezi; ndipo machimo anu akumanitsani zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphulupulu zanu zacotsa zimenezi, ndi zocimwa zanu zakukanitsani inu zinthu zabwino.