Jeremiah 5:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense ankathamangira mkazi wa mnzake, monga amachitira akavalo onenepa akamamemesa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anali onga akavalo okhuta mamawa; yense wakumemesera mkazi wa mnansi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga amachitira akavalo onenepa akamamemesa, aliyense wa iwo ankathamangira mkazi wa mnzake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anali onga akavalo okhuta mamawa; yense wakumemesera mkazi wa mnansi wace.