Jeremiah 50:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naŵa mau amene Chauta adalankhula ndi mneneri Yeremiya kunena za mzinda wa Babiloni ndi anthu ake. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau amene ananena Yehova za Babiloni, za dziko la Ababiloni, mwa Yeremiya mneneri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uthenga umene Yehova anayankhula ndi mneneri Yeremiya wonena za mzinda wa Babuloni ndi anthu ake ndi uwu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau amene ananena Yehova za Babulo, za dziko la Akasidi, mwa Yeremiya mneneri.