Jeremiah 50:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Lithireni nkhondo dziko la Merataimu ndi anthu okhala ku Pekodi. Muŵaphe ndi lupanga ndi kuŵaonongeratu. Muchite zonse zimene ndakulamulani,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwera kukamenyana ndi dziko la Merataimu, ndi okhala m'Pekodi, ipha nuononge konse pambuyo pao, ati Yehova, chita monga mwa zonse ndinakuuza iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Lithireni nkhondo dziko la Merataimu ndi anthu okhala ku Pekodi. Muwaphe ndi lupanga ndi kuwawonongeratu,” akutero Yehova. “Chitani zonse monga momwe ndakulamulani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwera kukamenyana ndi dziko la Merataimu, ndi okhala m'Pekoli, ipha nuononge konse pambuyo pao, ati Yehova, cita monga mwa zonse ndinakuuza iwe.