Jeremiah 50:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta watsekula nyumba ya zida zake, ndipo watulutsa zida za mkwiyo wake. Paja Chauta Wamphamvuzonse ali ndi ntchito yoti agwire ku dziko la Ababiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova watsegula pa nyumba ya zida zake, ndipo watulutsa zida za mkwiyo wake; pakuti Ambuye Yehova wa makamu, ali ndi ntchito m'dziko la Ababiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova watsekula nyumba ya zida zake ndipo watulutsa zida za ukali wake, pakuti Ambuye Yehova Wamphamvuzonse ali ndi ntchito yoti agwire mʼdziko la Ababuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova watsegula pa nyumba ya zida zace, ndipo waturutsa zida za mkwiyo wace; pakuti Ambuye Yehova wa makamu, ali ndi nchito m'dziko la Akasidi.