Jeremiah 50:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iphani anyamata ake onse ankhondo. Onse aphedwe ndithu. Tsoka laŵagwera pakuti tsiku lao la chilango lafika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iphani ng'ombe zamphongo zake zonse; zitsikire kukaphedwa; tsoka iwo! Pakuti tsiku lao lafika, tsiku la kulanga kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iphani ankhondo ake onse. Onse aphedwe ndithu. Tsoka lawagwera pakuti tsiku lawo lachilango lafika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iphani ng'ombe zamphongo zace zonse; zitsikire kukaphedwa; tsoka iwo! pakuti tsiku lao lafika, tsiku la kulanga kwao.