Jeremiah 50:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndikumva anthu othaŵa nkhondo ya ku Babiloni akulengeza za kulipsira kwa Chauta, Mulungu wathu, kulipsirira chifukwa choononga Nyumba yake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a iwo akuthawa akupulumuka m'dziko la Babiloni, kuti alalikire m'Ziyoni kubwezera chilango kwa Yehova Mulungu wathu, kubwezera chilango chifukwa cha Kachisi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tikumva anthu othawa nkhondo ochokera ku Babuloni akulengeza mu Yerusalemu za kulipsira kwa Yehova Mulungu wathu. Iye akulipsira chifukwa chowononga Nyumba yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a iwo akuthawa akupulumuka m'dziko la Babulo, kuti alalikire m'Ziyoni kubwezera cilango kwa Yehova Mulungu wathu, kubwezera cilango cifukwa ca Kacisi wace.