Jeremiah 50:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mtundu wa anthu akumpoto wadzauthira nkhondo mzinda wa Babiloni. Dziko lake adzalisandutsa bwinja, ndipo kumeneko sikudzakhalanso munthu kapena nyama.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mtundu wa anthu udzatuluka kumpoto kudzamenyana naye, udzachititsa dziko lake bwinja, losakhalamo anthu; athawa, apita, anthu ndi nyama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtundu wa anthu wochokera kumpoto wadzathira nkhondo Babuloni ndi kusandutsa bwinja dziko lake. Kumeneko sikudzakhalanso munthu kapena nyama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mtundu wa anthu udzaturuka kumpoto kudzamenyana naye, udzacititsa dziko lace bwinja, losakhalamo anthu; athawa, apita, anthu ndi nyama.