Jeremiah 50:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Lupanga lankhondo lilunjika pa Ababiloni, Imfa iloze pa anthu a ku Babiloni, pa akuluakulu ao ndi pa anthu ao anzeru,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lupanga lili pa Ababiloni, ati Yehova, pa okhala m'Babiloni, pa akulu ake, ndi pa anzeru ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Imfa yalunjika pa Ababuloni, pa akuluakulu ake ndi pa anthu ake a nzeru!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lupanga liri pa Akasidi, ati Yehova, pa okhala m'Babulo, pa akuru ace, ndi pa anzeru ace.