Jeremiah 50:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Lupanga lilunjike pa anthu oombeza, kuti asanduke zitsilu. Lilunjikenso pa ankhondo ake, kuti aonongedwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lupanga lili pa amatukutuku, ndipo adzapusa; lupanga lili pa anthu olimba ake, ndipo adzaopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imfa yalunjika pa aneneri abodza kuti asanduke zitsiru. Imfa yalunjika pa ankhondo ake kuti agwidwe ndi mantha aakulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lupanga liri pa amatukutuku, ndipo adzapusa; lupanga liri pa anthu olimba ace, ndipo adzaopa.