Jeremiah 50:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe Mulungu adaonongera Sodomu ndi Gomora ndi mizinda yonse yozungulira, momwemonso palibe munthu amene adzakhale kumeneko. Palibe ndi mmodzi yemwe amene azidzayendako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga muja Yehova anagwetsa Sodomu ndi Gomora ndi midzi inzake, ati Yehova; anthu sadzakhalamo, mwana wa munthu sadzagonamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora pamodzi ndi mizinda yonse yozungulira,” akutero Yehova, “momwemonso palibe amene adzakhale kumeneko; anthu sadzayendanso mʼmenemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga muja Yehova anagwetsa Sodomu ndi Gomora ndi midzi Inzace, ati Yehova; anthu sadzakhalamo, mwana wa munthu sadzagonamo.