Jeremiah 50:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Thaŵaniko ku Babiloni. Chokaniko ku dziko la Ababiloni, muyambe ndinu kutuluka, ngati atonde otsogolera ziŵeto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thawani pakati pa Babiloni, tulukani m'dziko la Ababiloni, mukhale monga atonde patsogolo pa zoweta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Thawaniko ku Babuloni; chokani mʼdziko la Ababuloni. Muyambe inu kutuluka ngati atonde amene amatsogolera ziweto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thawani pakati pa Babulo, turukani m'dziko la Akasidi, mukhale monga atonde patsogolo pa zoweta.