Jeremiah 51:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Ndidzautsa mphepo yoti idzaononge Babiloni pamodzi ndi onse okhala m'dziko la Babiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova atero: Taonani, ndidzaukitsira Babiloni, ndi iwo okhala m'Lebi-kamai, mphepo yoononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Taonani, ndidzadzutsa mphepo yowononga kuti iwononge Babuloni pamodzi ndi anthu a ku Lebi Kamai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova atero: Taonani, ndidzaukitsira Babulo, ndi iwo okhala m'Lebi-kamai, mphepo yoononga,