Jeremiah 51:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu amene muli ndi mitsinje yambiri, ndinu olemera kwambiri, koma chimalizo chanu chafika, moyo wanu watha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe wokhala pa madzi ambiri, wochuluka chuma, chimaliziro chako chafika, chilekezero cha kusirira kwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu muli ndi mitsinje yambiri ndi chuma chambiri. Koma chimaliziro chanu chafika, moyo wanu watha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe wokhala pa madzi ambiri, wocuruka cuma, cimariziro cako cafika, cilekezero ca kusirira kwako.