Jeremiah 51:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafanowo ngachabechabe, oyenera kuŵaseka, ndipo pamene anthuwo adzalangidwe, mafanowo adzaonongedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngwachabe, chiphamaso; nthawi ya kulangidwa kwao adzatayika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafanowo ndi achabechabe, zinthu zosekedwa nazo. Pamene anthuwo azidzaweruzidwa mafanowo adzawonongedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngwacabe, ciphamaso; nthawi yakulangidwa kwao adzatayika.