Jeremiah 51:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe mwala wako ndi umodzi womwe umene adzabwere nawo kuti augwiritse ntchito ngati mwala wapangodya. Iwe udzakhala chipululu mpaka muyaya,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sadzachotsa pa iwe mwala wa pangodya, kapena mwala wa pamaziko; koma udzakhala bwinja nthawi zonse, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe ngakhale ndi mwala wako umodzi umene anthu adzawutenga kuti awugwiritse ntchito kumangira nyumba, chifukwa iwe udzakhala chipululu mpaka muyaya,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sadzacotsa pa iwe mwala wa pangondya, kapena mwala wa pamaziko; koma udzakhala bwinja nthawi zonse, ati Yehova.