Jeremiah 51:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Othamanga akungopezanapezana, amithenganso akungotsatanatsatana. Onsewo akukauza mfumu ya ku Babiloni kuti mbali zonse za mzinda wake zalandidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wamtokoma mmodzi adzathamanga kukakomana ndi mnzake, ndi mthenga mmodzi kukomana ndi mnzake, kukauza mfumu ya ku Babiloni kuti mudzi wake wagwidwa ponsepo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Othamanga akungopezanapezana, amithenga akungotsatanatsatana kudzawuza mfumu ya ku Babuloni kuti alande mzinda wake wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wamtokoma mmodzi adzathamanga kukakomana ndi mnzace, ndi mthenga mmodzi kukomana ndi mnzace, kukauza mfumu ya ku Babulo kuti mudzi wace wagwidwa ponsepo;