Jeremiah 51:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzapita nawo kuti akaphedwe ngati anaankhosa, ngati nkhosa zamphongo kapena atonde,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzawagwetsa kuti aphedwe monga anaankhosa amphongo, ndi atonde.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine ndidzawatenga kuti akaphedwe ngati ana ankhosa onenepa, ngati nkhosa zazimuna ndi mbuzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzawagwetsa kuti aphedwe manga nkhosa zamphongo, ndi atonde.