Jeremiah 51:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndithu Babiloni wagonjetsedwa, mzinda umene dziko lonse lapansi linkaunyadira walandidwa. Ogo! Babiloni uja wasanduka chinthu chonyansa pakati pa mitundu ya anthu!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sesaki wagwidwatu! Chimene dziko lonse lapansi linachitamanda chalandidwa dzidzidzi! Babiloni wakhalatu bwinja pakati pa amitundu!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndithu Babuloni walandidwa, mzinda umene dziko lonse lapansi limanyadira wagwidwa! Taonani, mmene Babuloni wasandukira chinthu chochititsa mantha pakati pa mitundu ya anthu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sesake wagwidwatul cimene dziko lonse lapansi linacitamanda calandidwa dzidzidzi Babulo wakhalatu bwinja pakati pa amitundu