Jeremiah 51:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyanja yakwera mpaka kumiza Babiloni, waphimbidwa ndi mafunde ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyanja yakwera kufikira ku Babiloni; wamira ndi mafunde ake aunyinji.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyanja yakwera ndi kumiza Babuloni; mafunde ake okokoma aphimba Babuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyanja yakwera kufikira ku Babulo; wamira ndi mafunde ace aunyinji.