Jeremiah 51:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tulukani m'Babiloni, inu anthu anga! Fulumirani, pulumutsani moyo wanu! Thaŵani mkwiyo woopsa wa Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu anga, tulukani pakati pake, mudzipulumutse munthu yense ku mkwiyo waukali wa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tulukani mʼBabuloni anthu anga! Pulumutsani miyoyo yanu! Thawani mkwiyo woopsa wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu anga, turukani pakati pace, mudzipulumutse munthu yense ku mkwiyo waukali wa Yehova.