Jeremiah 51:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake dziko lakumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zokhala m'menemo zidzaimba mokondwera chifukwa cha kugwa kwa Babiloni. Anthu oononga ochokera kumpoto adzamgonjetsa,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo kumwamba ndi dziko lapansi, ndi zonse zili m'menemo, zidzaimba mokondwerera Babiloni; pakuti akufunkha adzafika kwa iye kuchokera kumpoto, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mʼmenemo zidzayimba mokondwa chifukwa cha kugwa kwa Babuloni. Anthu owononga ochokera kumpoto adzamuthira nkhondo,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo kumwamba ndi dziko lapansi, ndi zonse ziri m'menemo, zidzayimba mokondwerera Babulo; pakuti akufunkha adzafika kwa iye kucokera kumpoto, ati Yehova.