Jeremiah 51:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Babiloni ayeneradi kugwa chifukwa cha amene adaphedwa ku Israele, monga adagwera anthu a pa dziko lonse lapansi amene adaphedwa ndi iyeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga Babiloni wagwetsa ophedwa a Israele, momwemo pa Babiloni padzagwa ophedwa a dziko lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Babuloni anapha anthu ambiri pa dziko lapansi. Tsono, nawo anthu a ku Babuloni ayenera kuphedwa chifukwa anapha anthu a ku Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga Babulo wagwetsa ophedwa a Israyeli, momwemo pa Babulo padzagwa ophedwa a dziko lonse.