Jeremiah 51:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta akunena kuti, “Ikubwera nthaŵi pamene ndidzalange mafano a ku Babiloni, ndipo kubuula kwa anthu olasidwa kudzamveka m'dziko lake lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake, taona, masiku alinkudza, ati Yehova, amene ndidzaweruza mafano ake; ndipo pa dziko lake lonse olasidwa adzabuula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake Yehova akuti, “Masiku akubwera pamene ndidzalanga mafano ake, ndipo mʼdziko lake lonse anthu ovulala adzabuwula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace, taona, masiku alinkudza, ati Yehova, amene ndidzaweruza mafano ace; ndipo pa dziko lace lonse olasidwa adzabuula.