Jeremiah 51:63 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukakatha kuŵerenga bukulo, ukalimangire ku mwala, nkuliponya mu mtsinje wa Yufurate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzakhala, utatha kuwerenga buku ili, ulimange ndi mwala, nuliponye pakati pa Yufurate;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukakatha kuwerenga bukuli, ukalimangirire ku mwala ndipo ukaliponye pakati pa mtsinje wa Yufurate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzakhala, utatha kuwerenga buku ili, Ib ulimange ndi mwala, nuliponye pakati pa Firate;