Jeremiah 51:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Babiloni wagwa mwadzidzidzi ndipo waonongeka. Mlireni, mfunireni mankhwala, kuti mwina nkuchira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Babiloni wagwa dzidzidzi naonongedwa; mumkuwire iye; mutengere zowawa zake vunguti, kapena angachire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Babuloni wagwa mwadzidzidzi ndi kusweka. Mulireni! Mfunireni mankhwala opha ululu wake; mwina iye nʼkuchira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Babulo wagwa dzidzidzi naonongedwa; mumkuwire iye; mutengere zowawa zace bvunguti, kapena angacire.