Jeremiah 52:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nsanamira ziŵiri zija, chimbiya, maphaka ndiponso ng'ombe zamphongo khumi ndi ziŵiri zimene zinkachirikiza chimbiyacho, zimene mfumu Solomoni adaapangira Nyumba ya Chauta kulemera kwake kwa mkuŵa wa zonsezo kunali kosaŵerengeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsanamira ziwirizo, thawale limodzilo, ndi ng'ombe zamkuwa zinali pansi pa zoikapo, zimene mfumu Solomoni anazipangira nyumba ya Yehova; mkuwa wa zipangizo zonsezi sanathe kuyesa kulemera kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nsanamira ziwiri zija, chimbiya, maphaka ndi ngʼombe khumi ndi ziwiri za mkuwa zochirikizira chimbiyacho zimene mfumu Solomoni anapangira Nyumba ya Yehova kulemera kwake kunali kosawerengeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsanamira ziwirizo, thawale limodzilo, ndi ng'ombe zamkuwa zinali pansi pa zoikapo, zimene mfumu Solomo anazipangira nyumba ya Yehova; mkuwa wa zipangizo zonsezi sanatha kuyesa kulemera kwace.