Jeremiah 52:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Nebuzaradani mkulu wa asilikali uja, adagwira Seraya mkulu wa ansembe ndi Zefaniya, wachiŵiri kwa mkulu wa ansembe, ndi alonda atatu apachipata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kapitao wa alonda anatenga Seraya wansembe wamkulu, ndi Zefaniya wansembe wachiwiri, ndi akudikira pakhomo atatu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsogoleri wa ankhondo uja, anagwira Seraya mkulu wa ansembe ndi Zefaniya, wachiwiri wa mkulu wa ansembe ndi alonda atatu apachipata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kapitao wa alonda anatenga Seraya mkuru wansembe, ndi Zefaniya wansembe waciwiri, ndi akudikira pakhomo atatu;