Jeremiah 52:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nebuzaradani, mkulu wa asilikali uja, adaŵatenga onsewo napita nawo kwa mfumu ya ku Babiloni ku Ribula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Nebuzaradani kapitao wa alonda anatenga iwo, nadza nao kwa mfumu ya ku Babiloni ku Ribula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nebuzaradani, mtsogoleri wa ankhondoyo anawatenga onse napita nawo kwa mfumu ya ku Babuloni ku Ribula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Nebuzaradani kapitao wa alonda anatenga iwo, nadza nao kwa mfumu ya ku Babulo ku Ribila.