Jeremiah 52:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalankhula naye mwachifundo, nampatsa malo aulemu kuposa mafumu ena amene anali naye ku Babiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena naye bwino, naika mpando wake upose mipando ya mafumu amene anali naye m'Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Evili-Merodaki anakomera mtima Yehoyakini, namupatsa malo aulemu kuposa mafumu ena amene anali naye ku Babuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena naye bwino, naika mpando wace upose mipando ya mafumu amene anali naye m'Babulo.