Jeremiah 52:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena za phoso, mfumu ya ku Babiloni inkampatsa Yehoyakimu phoso lake tsiku ndi tsiku mpaka kufa kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma phoso lake mfumu ya ku Babiloni sanaleke kumpatsa, phoso tsiku ndi tsiku gawo lake, mpaka tsiku la kufa kwake, masiku onse a moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku ndi tsiku mfumu ya ku Babuloni inkamupatsa Yehoyakini phoso lake nthawi yonse ya moyo wake, mpaka pa nthawi ya imfa yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma phoso lace mfumu ya ku Babulo sanaleka kumpatsa, phoso tsiku ndi tsiku gawo lace, mpaka tsiku la kufa kwace, masiku onse a moyo wace.